Auteur : Damazio Phiri
Coordonnateurs : Jean-Luc Taradel et Aurélie Layemard
FRANÇAIS | NYANJA |
acheteur | ogura |
acteur planétaire | munthu ochita masewero pa malo ochitira ya anthu onse |
affaires | malonda |
aide en ligne | thandizo la pa Intaneti |
album de presse | buku la amtola nkhani |
argent du cœur | konda ndalama |
arrosage | kuthilira |
attaquant | wakuba |
au revoir | tsalani bwino |
banque de données | mbili ya bank |
besoins | zofunika |
bonjour | mwauka bwanji |
Bourse | kusintha kwa zinthu pa za malonda |
boutique hors taxes | sitolo losapereka msonkho mwalamulo |
capacité d’autofinancement | ndalama zolowa |
capital-risque | ndalama zoyambira malonda |
capitaux flottants | ndalama ya mphamvu kwambiri |
centre commercial | malo ochitira malonda amasitolo |
centre d’affaires international | likulu la msika wa dziko lonse |
chaîne logistique | njira yopanga dongosolo |
chevalier blanc | usiku wabwino |
chevalier noir | usiku oipa |
client | kastomala |
coentreprise | malonda ochitira pamodzi |
cœur de métier | kuchita zinthu mofunika |
commerce | malonda |
commerce en ligne | malonda a pa intaneti |
commerce équitable | malonda ochitiwa bwino |
comptant | ndalama |
conditions internationales de vente (CIV) | malamulo a malonda akunja kwa dziko |
contrat | pangano |
coopérative | chigwirizano |
coucounage | kuteteza |
courriel | kalata ya email |
crédit-bail | kubwereketsa |
crédit de restructuration | ndalama yatsopano |
crédit ponctuel | nkhongole zosatengedwa bwino |
culture d’entreprise | chikhalidwe cha chigwilizano |
cyberespace | zopezeka pa computer zochedwa cyberspace |
cybermercaticien | katswiri pa msika wa zokambilana pa makina a computer pa cyber |
demande | zolemba zofuna |
dénicheur | ogwira nchito bwino |
développement durable | chitukuko chokhazikika |
discompteur | obwezako mtengo |
distribution | gawanitsa |
échange financier | sinthanitsana |
économie de marché | maziko a chuma cha msika |
économie en réseau | maziko a chuma pa njira yokambilana |
économie sociale | maziko a chuma pa chikhalidwe |
entreprise | malonda |
entreprise à consommateur en ligne | malonda kufika ku ogula |
essaimage | kuzungulutsa |
éthique des affaires | lamulo la malonda |
étude de marché | kufufudza za msika |
externalisation | kufufuna ndi kupeza malonda |
fabriqué en, à, au… | kupangidwa mu… |
flux de trésorerie | ndalama zolowa |
franchisage | chilolezo |
gagnant-gagnant | kupambana-kupambana |
gestion | kayendetsedwe |
gestion des relations avec la clientèle | kudziwa kukambilana ndi makastomala |
gestion du savoir | kugwilitsa nchito nzeru |
groupe de pression | gulu |
homme (femme) d’affaires | munthu wa nchito za malonda mwamuna kapena mkazi |
hypermarché | sitolo la hypermarket |
information en ligne | mbiri pa zokambilana za pa makina a computer kudzera mu cyber |
investisseur providentiel | mponda matiki wabwino wa nchito za malonda |
je parle votre (ta) langue | ndilankhula chilankhulo chanu |
jeune pousse | zomera zing`no zing`ono |
lèche-vitrines | kuona malonda koma osagula |
libre-service | kuzichitira pa yekha |
location avec option d’achat | kubwereketsa |
logiciel | pologilamu ya mu makina a compyuta |
magasin d’exposition | chipinda cha chiwonetsero |
magasin d’usine | ntambi ya fakitare |
manageur | mkulu wa nchito |
marchandisation | kusintha kukhala katundu |
marché | msika |
marchéage | kusakaniza kwa za msika |
marge brute d’autofinancement | ndalama zolowa |
mentor | ounikira |
mercaticien | katswiri wa za msika |
mercatique | kutsatsa malonda |
merci | zikomo |
mutuelle | kampani yopereka chitetezo |
navetteur | okwera magalimoto, masitima |
négociant | munthu wa nchito za malonda |
offre | msika |
parrainage | kukhalira kumbuyo |
parraineur | othandiza kupereka malonda patsogolo |
personnalisation | chifanizo |
picoreur | opeza phindu mwachinyengo |
plan d’affaires | pulano la malonda |
post-marché | ofesi la chisinsi |
poulain | kugwilitsa nchito chinthu molakwikwa |
prix réduit | kubwezako mtengo |
produit | katundu |
publipostage | kulengeza makalata |
rapport (compte rendu) social | kulengeza pa za chikhalidwe |
redevance | ndalama zolipira |
remue-méninges | kusinkhasikha |
réponse optimale au consommateur | kuyankha kastomala mofunikira |
restauration rapide | malonda a chakudya chofunika musanga |
résultat net d’exploitation | ndalama zopezeka pambuyo nkhoma msonkho |
rotation | kuzungulira |
salle des marchés | chipinda chicitira malonda |
sans usine | palibe fakitare la zomera |
savoir-faire | kudziwa |
service au volant | nchito yozungulira |
service d’appui | nchito yothandizira |
service de clientèle | nchito yothandizira makastomala |
société (commerciale) | kampani |
supermarché | sitolo la supermarket |
surréservation | upezelatu malo ya ambiri |
technique de pointe | kuya pa za makina |
téléachat | kugulu kogwiritsa nchito lamya |
télémarché | msika wa pa lamya |
télétravailleur | kukonzekera ulendo pogwiritsa nchito lamya |
tenante | mwini wa |
tendance structurelle | njira yoendetsera zinthu |
Toile | njira yogwilizirana ya pa internet |
tontine | kusonka |
valeur vedette | kukhala ndi katundu wa malonda mwamatsenga |
veille économique | kudzuka kwa maziko a chuma |
vendeur | munthu ogulitsa |
voyagiste | wa nchito yoendera |
zone euro | dera la euro |
Note : le nyanja (appelé aussi chinyanja, chewa et chichewa) appartient à la famille des langues bantoues. C’est la langue nationale du Malawi et une des sept langues officielles africaines de la Zambie. Il est aussi parlé au Mozambique et au Zimbabwe.
Si vous avez remarqué une erreur ou un oubli, ayez l’obligeance de nous en informer en envoyant un message au responsable du site.